Chuma
Kodi Yesu ndi yani kwa inu? Yankho yanu kwa iyi funso
ingathe kusintha umoyo wanu kwa nthawi zosathata.
Pali zoona zazikulu zinai zofunika kuti
mudziziwe ndi kuzisamala kuti mukhale ndi moyo weni-weni wabwino.
Tsiku ndi tsiku ingathe kukhala yokondwelesa kwa Mkristu
amene adziwa tanthauzo yoyenda mu Mzimu Oyera.
Kanaema ya mola awiri ya Umoyo wa Yesu kristu yolembedwa
ndi Luka, icedwa kanema yopambana konse inapagidwa pa kusonyeza
umoyo wa Yesun Kristu wa ku Nazareti.T
|