Chichewa Malankhulidwe ena
Yanjanani ndi ena ambiri amene aona Ulemelero wa Yesu Kristu, ndipo moyo wao wasinthidwa kwatsiku zosatha.

Kanema ya YESU
Real Vidiyo

Kanema ya YESU ndi yodabwitsa! Iyi kanema ni ndendede na zolembedwa mu Baibulo mu Buku ya Luka. Umoyo wa Yesu kristu, macitidwe ace, zodzizditwa zace, zonsezi miziona mu kanema iyi.  Ndipo mphavu ya Mulungu imugwilanai pamene mucitila umboni wa Yesu Kristu.

Yanjanani ndi ena ambiri amene aona ulemelero wa Yesu Kristu, ndipo moyo wao wasinthidwa kwa nthawi zosatha. Kanemayi yijambulidwa mu mdziko ya Iraeli.

Kanema iyi ya YESU  itha kusintha moyo wanu kwa nthawi yosatha.

IKuti muone iyi kanema muyenela kukhala ndi  RealPlayer yomwe mutha kutenga ku:  Progressive Networks (http://www.real.com/).

Mungathe Kugula Iyi Kanema pa Vidiyo

Home Yesu Ndi Yani? Kanema ya YESU Malamulo Anai Moyo wa Uzimu Mwayi Chuma

© 2002 Campus Crusade for Christ International

Last Updated: 14 March, 2002