Mungathe kupika ku dziko lililonse kapena kulankhula
ndi anthu a mipingo yosina-siyana ngakhale ndi odzipeleka ku mupingo wao.
Komabe adzavomela kuti kulibe munthu wina opotsa Yesu Kristu waku
Nazareti. Moyo wace unali odabwistsa kwabasi.
KUBWELA
KWAKE KUNALONJEZEDWA
Zikwi-zikwi, pomwe Yesu sanabadwe, Malembo Oyera atiudza za aneneli a
Israyeli akulonjeza kubwela kwa Yesu. Cipangano cakale mu Buku
Lopatulika, cinalembedwa ndi aneneri ambiri kwa dzaka zikwi khumi ndi
zisanu kulonjeza kubwela kwace. Zonse zomwe zinalembedwa
dzinafikilisidwa.
Moyo wace, zodzidzitswa zace, mau ace, infa yace, ku-ukitsidwa kwa akufa
kwace ndi kupita kumwamba kwace, zonse zisonyeza kuti Yesu anali mwana wa
Mulungu. Yesu anati "Ine ndi Atate tili m'modzi" (Yohane10:30),
"Iye amene waona ine anona Atate" (Yohane 14:9). Yesu
anati "Inen dine njira coonadi ndi moyo, kulibe obwela kwa Atate kopanda
ine" (Yohane 14:6).
MOYO NDI UTHENGA WACE
Onani moyo, uthenga ndi macitidwe a Yesu Kristu. Anthu
ambirir-mbiri akhala akusintha cifukwa ca moyo wa Yesu Kristu. Kuli
konse komwe uthenga ndi maphunzintso ace apita anthu amitundu yonse asintha.
YESU ANAUKA KWA AKUFA
Yesu Kristu anapacikidwa pa mtanda, naikidwa m'manda, ndipo tsuku
yacitatu anauka kwa akufa. Cikristu ndicodabwitsa cifukwa ca ku
ukitsidwa kwa Yesu kristu.
Zaka zambiri zapitapo, ndipo anthu ophunzira ambiri azindikira ndi
kucitira umboni kuti Yesu Kristu alimoyo."
John Singleton Copley, mtsogoleri wa opuhunzira ku mangalande anati,
"Ndizindkila kuti Yesu anauka kwa akufa ndipo zimenedzi
sidzitsusidwa ayi."
NICIFUKWA NINJI TIKHULUPIRIRA?
Kuukisidwa kwa akufa kwa Yesus Kristu ndi kwakukulu kwa a Kristu aonse.
Ndipo ife tikhulupirira cifukwa ca izi:
KUNALONJEZEDWA:
Coyamba, Yesu Kristu mwini ananena za infa yace ndi ku-uka kwa akufa kwace
pamene nthawi sinafike (Luka18:31-33)
MANDA ACE ANALIBE KANTHU:
Caciwiri, m'manda momwe munaikidwa mtembo wace munalibe pa tsiku yacitatu.
Ici cisonyeza kuti Yesu anadzuka. Baibulo limatiuza ife kuti
asilikali anaikidwa kuonela manda ndipo cimwala cacikula cinaikidwa
pakhomo pamandayo. Mtembo wa yesu sinabedweayi, koma iye anauka kwa akufa.
ANAONEKELA KWA IWO:Cacitatu, Yesu Kristu anaonekela kwa
omphunzira ace ndi kwa anthu ambiri-mbiri (500) pa nthawi imodzi, pamene iye
anadzuka. Yesu anaonetselatu kuti iye ndwmoyo ndipo iye anadya
naocakudya.
KUBADWA KWA MUPINGO(CHALICI): Cacinai, kuuka kwa Yesu
kristu kwa akufa ndiko kubadwa kwa mpingo (Chalici). Chalici ya Akristu
ndi mpingo ukulu opambana pa dziko lonse lapansi .
MOYO WATSOPANO:
Dziko lonse lapansi, anthu osiyana-siyana akhla akupeza mtendere pamena
aika cikhulupiriro cao mwa Yesu Kristu. Kulibe munthu atha kusintha
moyo wa anthu monga Yesu kristu. Zonsezi zicitira umboni ku coondi
coti Yesu Kristu ali moyo lelo ndipo iye anauka kwa akufa.
MFUMU
YA MOYO:
Cifukwa cakuukitsidwa kwa Yesu Kristu kwa akufa, onse ophunzira
ace akhulupirira muli Ambuye ndi Mfumu lamoyo. Kalelo, Yesu alimoyo
ndipo apatsa moyo weni-weni ndi ocuruka kwa yense okhulupirira mwa iye.
Ambiri avomela ndi kucitira umboni kuuka kwa Yesu Kristu ngakhale manfumu
ndi atsogoleri ocukha pa dziko lapansi.
Kodi mungakonde kumudziwa Yesu Kristu, kuti
iye akhale bwenzi lanu ndi kukupatsani moyo weni-weni ocuruka? Yesu
afunitsitsa kumupatsani Moyo ocuruka.
Ngati mufuna kuti Yesu akhale mpulumutsi ndi mtsogoleri wanu, dinizani
apa... |